Yohane 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Atate amalemekezeka mukapitiriza kubala zipatso zambiri ndi kusonyeza kuti mulidi ophunzira anga.+