Maliko 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tsopano anapitiriza ulendo wawo wopita ku Yerusalemu. Yesu anali patsogolo pawo, ndipo iwo anadabwa kwambiri. Anthu amene anali kum’tsatirawo anayamba kuchita mantha. Pamenepanso anatengera pambali ophunzira 12 aja ndi kuyamba kuwauza zinthu izi zimene zinali pafupi kum’chitikira:+ Luka 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako anatengera pambali ophunzira 12 aja ndi kuwauza kuti: “Tamverani! Tsopano tikupita ku Yerusalemu, ndipo zonse zimene zinalembedwa ndi aneneri,+ zokhudza Mwana wa munthu zikakwaniritsidwa.+
32 Tsopano anapitiriza ulendo wawo wopita ku Yerusalemu. Yesu anali patsogolo pawo, ndipo iwo anadabwa kwambiri. Anthu amene anali kum’tsatirawo anayamba kuchita mantha. Pamenepanso anatengera pambali ophunzira 12 aja ndi kuyamba kuwauza zinthu izi zimene zinali pafupi kum’chitikira:+
31 Kenako anatengera pambali ophunzira 12 aja ndi kuwauza kuti: “Tamverani! Tsopano tikupita ku Yerusalemu, ndipo zonse zimene zinalembedwa ndi aneneri,+ zokhudza Mwana wa munthu zikakwaniritsidwa.+