Maliko 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Koma Yakobo ndi Yohane, ana aamuna awiri a Zebedayo,+ anapita kwa iye ndi kumuuza kuti: “Mphunzitsi, tikufuna mutichitire chimene tikupempheni.”+
35 Koma Yakobo ndi Yohane, ana aamuna awiri a Zebedayo,+ anapita kwa iye ndi kumuuza kuti: “Mphunzitsi, tikufuna mutichitire chimene tikupempheni.”+