Maliko 10:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Tsopano ophunzira 10 ena aja atamva zimenezi, anakwiya kwambiri ndi Yakobo ndi Yohane.+ Luka 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Komanso, panabuka mkangano woopsa pakati pawo za amene anali kuoneka wamkulu kwambiri.+