Maliko 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Choncho anakhala pansi ndi kuitana ophunzira 12 aja ndi kuwauza kuti: “Ngati aliyense akufuna kukhala woyamba, ayenera kukhala wotsiriza pa onse, ndiponso mtumiki wa onse.”+ Maliko 10:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Amene akufuna kukhala woyamba pakati panu ayenera kukhala kapolo wa onse.+
35 Choncho anakhala pansi ndi kuitana ophunzira 12 aja ndi kuwauza kuti: “Ngati aliyense akufuna kukhala woyamba, ayenera kukhala wotsiriza pa onse, ndiponso mtumiki wa onse.”+