Maliko 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo analowa mu Yerusalemu, ndi kufika m’kachisi. Ndiyeno anayang’anayang’ana zinthu zonse, koma popeza nthawi inali itatha kale, anapita ku Betaniya limodzi ndi ophunzira ake 12 aja.+
11 Pamenepo analowa mu Yerusalemu, ndi kufika m’kachisi. Ndiyeno anayang’anayang’ana zinthu zonse, koma popeza nthawi inali itatha kale, anapita ku Betaniya limodzi ndi ophunzira ake 12 aja.+