Maliko 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako anafikanso ku Yerusalemu. Koma pamene anali kuyenda m’kachisi, ansembe aakulu, alembi ndi akulu anabwera kwa iye.+ Luka 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsiku lina pamene anali kuphunzitsa anthu m’kachisi ndi kulengeza uthenga wabwino, panafika ansembe aakulu, alembi pamodzi ndi akulu.+
27 Kenako anafikanso ku Yerusalemu. Koma pamene anali kuyenda m’kachisi, ansembe aakulu, alembi ndi akulu anabwera kwa iye.+
20 Tsiku lina pamene anali kuphunzitsa anthu m’kachisi ndi kulengeza uthenga wabwino, panafika ansembe aakulu, alembi pamodzi ndi akulu.+