Mateyu 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano Yesu analowa m’kachisi, ndipo pamene anali kuphunzitsa, ansembe aakulu ndiponso akulu anabwera kwa iye ndi kumufunsa kuti:+ “Kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Ndipo ndani anakupatsani ulamuliro umenewu?”+ Luka 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsiku lina pamene anali kuphunzitsa anthu m’kachisi ndi kulengeza uthenga wabwino, panafika ansembe aakulu, alembi pamodzi ndi akulu.+
23 Tsopano Yesu analowa m’kachisi, ndipo pamene anali kuphunzitsa, ansembe aakulu ndiponso akulu anabwera kwa iye ndi kumufunsa kuti:+ “Kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Ndipo ndani anakupatsani ulamuliro umenewu?”+
20 Tsiku lina pamene anali kuphunzitsa anthu m’kachisi ndi kulengeza uthenga wabwino, panafika ansembe aakulu, alembi pamodzi ndi akulu.+