Ekisodo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Poyankha iye anati: “Anakuika iwe ndani kukhala kalonga ndi woweruza wathu?+ Kodi ukufuna kundipha mmene unaphera Mwiguputo uja?”+ Pamenepo Mose anachita mantha ndipo anati mumtima mwake: “Haa! Nkhani ija yadziwika.”+ Luka 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo anamufunsa kuti: “Tiuzeni, kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Kapena ndani amene anakupatsani ulamuliro umenewu?”+ Yohane 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Ayudawo anati: “Utionetsa chizindikiro+ chotani tsopano chosonyeza kuti uli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi?” Machitidwe 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno anaimika atumwiwo pakati pawo n’kuyamba kuwafunsa kuti: “Kodi mwachita zimenezi ndi ulamuliro uti kapena m’dzina la ndani?”+
14 Poyankha iye anati: “Anakuika iwe ndani kukhala kalonga ndi woweruza wathu?+ Kodi ukufuna kundipha mmene unaphera Mwiguputo uja?”+ Pamenepo Mose anachita mantha ndipo anati mumtima mwake: “Haa! Nkhani ija yadziwika.”+
2 Iwo anamufunsa kuti: “Tiuzeni, kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Kapena ndani amene anakupatsani ulamuliro umenewu?”+
18 Koma Ayudawo anati: “Utionetsa chizindikiro+ chotani tsopano chosonyeza kuti uli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi?”
7 Ndiyeno anaimika atumwiwo pakati pawo n’kuyamba kuwafunsa kuti: “Kodi mwachita zimenezi ndi ulamuliro uti kapena m’dzina la ndani?”+