Luka 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma onse mofanana anayamba kupereka zifukwa zokanira.+ Woyamba anamuuza kuti, ‘Ine ndagula munda, choncho ndiyenera kupita kukauona. Pepani sinditha kufika!’+
18 Koma onse mofanana anayamba kupereka zifukwa zokanira.+ Woyamba anamuuza kuti, ‘Ine ndagula munda, choncho ndiyenera kupita kukauona. Pepani sinditha kufika!’+