Maliko 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Wofesayo amafesa mawu.+ Luka 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Wofesa mbewu anapita kukafesa mbewu zake. Pamene anali kufesa, zina zinagwera m’mbali mwa msewu ndipo zinapondedwapondedwa, kenako zinadyedwa ndi mbalame zam’mlengalenga.+
5 “Wofesa mbewu anapita kukafesa mbewu zake. Pamene anali kufesa, zina zinagwera m’mbali mwa msewu ndipo zinapondedwapondedwa, kenako zinadyedwa ndi mbalame zam’mlengalenga.+