Mateyu 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu aliyense akamva mawu a ufumu koma osazindikira tanthauzo lake, woipayo+ amabwera n’kukwatula zomwe zafesedwa mumtima wa munthuyo. Izi ndi zofesedwa m’mbali mwa msewu zija. 1 Petulo 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 koma mawu a Yehova amakhala kosatha.”+ “Mawu”+ amenewo ndi amene alengezedwa+ kwa inu monga uthenga wabwino.
19 Munthu aliyense akamva mawu a ufumu koma osazindikira tanthauzo lake, woipayo+ amabwera n’kukwatula zomwe zafesedwa mumtima wa munthuyo. Izi ndi zofesedwa m’mbali mwa msewu zija.
25 koma mawu a Yehova amakhala kosatha.”+ “Mawu”+ amenewo ndi amene alengezedwa+ kwa inu monga uthenga wabwino.