Mateyu 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno pamene analowa m’ngalawa,+ ophunzira ake anam’tsatira. Luka 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsiku lina m’masiku amenewo Yesu ndi ophunzira ake anakwera ngalawa, ndipo anawauza kuti: “Tiyeni tiwolokere tsidya lina la nyanja.” Pamenepo iwo anayamba kupalasa.+
22 Tsiku lina m’masiku amenewo Yesu ndi ophunzira ake anakwera ngalawa, ndipo anawauza kuti: “Tiyeni tiwolokere tsidya lina la nyanja.” Pamenepo iwo anayamba kupalasa.+