Luka 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsiku lina Yesu ndi ophunzira ake anakwera ngalawa ndipo anawauza kuti: “Tiyeni tiwolokere tsidya lina la nyanja.” Choncho iwo anayamba kupalasa.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:22 Yesu—Ndi Njira, tsa. 113 Nsanja ya Olonda,5/1/1987, tsa. 8
22 Tsiku lina Yesu ndi ophunzira ake anakwera ngalawa ndipo anawauza kuti: “Tiyeni tiwolokere tsidya lina la nyanja.” Choncho iwo anayamba kupalasa.+