Mateyu 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chotero amunawo anadabwa n’kunena kuti: “Kodi munthu ameneyu ndi wotani,+ moti ngakhale mphepo ndi nyanja zikum’mvera?” Luka 8:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno anawafunsa kuti: “Chikhulupiriro chanu chili kuti?” Koma iwo anagwidwa ndi mantha ndipo anathedwa nzeru, mwakuti anayamba kufunsana kuti: “Kodi ameneyu ndani kwenikweni, wochita kulamula mphepo ndi madzi ndipo n’kumumvera?”+ Yohane 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma atapalasa makilomita pafupifupi 5 kapena 6, anaona Yesu akuyenda panyanja, kuyandikira ngalawayo ndipo iwo anachita mantha.+
27 Chotero amunawo anadabwa n’kunena kuti: “Kodi munthu ameneyu ndi wotani,+ moti ngakhale mphepo ndi nyanja zikum’mvera?”
25 Ndiyeno anawafunsa kuti: “Chikhulupiriro chanu chili kuti?” Koma iwo anagwidwa ndi mantha ndipo anathedwa nzeru, mwakuti anayamba kufunsana kuti: “Kodi ameneyu ndani kwenikweni, wochita kulamula mphepo ndi madzi ndipo n’kumumvera?”+
19 Koma atapalasa makilomita pafupifupi 5 kapena 6, anaona Yesu akuyenda panyanja, kuyandikira ngalawayo ndipo iwo anachita mantha.+