Mateyu 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chotero amunawo anadabwa n’kunena kuti: “Kodi munthu ameneyu ndi wotani,+ moti ngakhale mphepo ndi nyanja zikum’mvera?” Maliko 4:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Koma iwo anagwidwa mantha aakulu, ndipo anayamba kufunsana kuti: “Kodi ameneyu ndani kwenikweni, chifukwa ngakhale mphepo ndi nyanja zikumumvera?”+
27 Chotero amunawo anadabwa n’kunena kuti: “Kodi munthu ameneyu ndi wotani,+ moti ngakhale mphepo ndi nyanja zikum’mvera?”
41 Koma iwo anagwidwa mantha aakulu, ndipo anayamba kufunsana kuti: “Kodi ameneyu ndani kwenikweni, chifukwa ngakhale mphepo ndi nyanja zikumumvera?”+