Mateyu 12:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ukatero umapita kukatenga mizimu ina 7 yoipa kwambiri kuposa umenewo.+ Ikalowa mkatimo imakhala mmenemo ndipo potsirizira pake zochita za munthuyo zimakhala zoipa kwambiri kuposa poyamba.+ Ndi mmenenso zidzakhalira ndi m’badwo woipawu.”+
45 Ukatero umapita kukatenga mizimu ina 7 yoipa kwambiri kuposa umenewo.+ Ikalowa mkatimo imakhala mmenemo ndipo potsirizira pake zochita za munthuyo zimakhala zoipa kwambiri kuposa poyamba.+ Ndi mmenenso zidzakhalira ndi m’badwo woipawu.”+