Luka 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yesu anamufunsa kuti: “Dzina lako ndani?” Iye anayankha kuti: “Khamu,” chifukwa mwa iye munalowa ziwanda zambiri.+
30 Yesu anamufunsa kuti: “Dzina lako ndani?” Iye anayankha kuti: “Khamu,” chifukwa mwa iye munalowa ziwanda zambiri.+