Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 8:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Koma amene anali kuyang’anira ziwetozo anathawa ndipo atalowa mumzinda anafotokoza zonse kuphatikizapo zimene zinachitikira amuna ogwidwa ndi ziwanda aja.

  • Luka 8:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Zitatero anthu anabwera kudzaona zomwe zachitikazo. Atafika kwa Yesu anapeza munthu amene anam’tulutsa ziwanda uja atakhala pansi pafupi ndi Yesu. Anamupeza atavala bwino komanso maganizo ake ali bwinobwino, ndipo iwo anachita mantha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena