-
Maliko 5:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Choncho anafika kwa Yesu, ndipo anaona munthu wogwidwa ndi chiwanda uja ali chikhalire, atavala bwino komanso maganizo ake ali bwinobwino, inde munthu uja amene anali ndi khamu la mizimu yonyansa. Pamenepo iwo anachita mantha.
-