Maliko 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yesu anapitiriza kuwauza kuti: “Mneneri salemekezedwa kwawo,+ ngakhale ndi achibale ake, ngakhale m’nyumba mwake momwe, koma kwina.”+
4 Koma Yesu anapitiriza kuwauza kuti: “Mneneri salemekezedwa kwawo,+ ngakhale ndi achibale ake, ngakhale m’nyumba mwake momwe, koma kwina.”+