Aroma 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti iye anauza Mose kuti: “Amene ndikufuna kumusonyeza chifundo, ndidzamusonyeza chifundo, ndipo ndidzamvera chisoni aliyense amene ndikufuna kumumvera chisoni.”+ Aefeso 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Mulungu, amene ndi wachifundo chochuluka,+ mwachikondi chake chachikulu chimene anatikonda nacho,+
15 Pakuti iye anauza Mose kuti: “Amene ndikufuna kumusonyeza chifundo, ndidzamusonyeza chifundo, ndipo ndidzamvera chisoni aliyense amene ndikufuna kumumvera chisoni.”+
4 Koma Mulungu, amene ndi wachifundo chochuluka,+ mwachikondi chake chachikulu chimene anatikonda nacho,+