Maliko 7:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano pobwerera kuchoka m’madera a Turo, anadutsa ku Sidoni ndi kufika kunyanja ya Galileya mpaka kukadutsa mkati mwa zigawo za Dekapole.+
31 Tsopano pobwerera kuchoka m’madera a Turo, anadutsa ku Sidoni ndi kufika kunyanja ya Galileya mpaka kukadutsa mkati mwa zigawo za Dekapole.+