Levitiko 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “‘Chilichonse chimene chingakhudze mnofu wake chidzakhala choyera,+ ndipo ngati munthu wadonthezera ena mwa magazi a nyamayo pachovala,+ chovala chimene wadonthezera magazicho muzichichapira kumalo oyera.+ Mateyu 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 chifukwa mumtima mwake anali kunena kuti: “Ndikangogwira malaya ake akunja okhawo, ndichira ndithu.”+
27 “‘Chilichonse chimene chingakhudze mnofu wake chidzakhala choyera,+ ndipo ngati munthu wadonthezera ena mwa magazi a nyamayo pachovala,+ chovala chimene wadonthezera magazicho muzichichapira kumalo oyera.+
21 chifukwa mumtima mwake anali kunena kuti: “Ndikangogwira malaya ake akunja okhawo, ndichira ndithu.”+