Mateyu 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye anawauza kuti: “Nditsatireni, ndipo ndikusandutsani asodzi a anthu.”+