Luka 8:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Mayiyo ataona kuti zimene wachitazo zadziwika anapita kwa Yesu akunjenjemera, ndipo anagwada ndi kuulula pamaso pa anthu onse chimene chinam’chititsa kuti amugwire, komanso mmene wachirira nthawi yomweyo.+
47 Mayiyo ataona kuti zimene wachitazo zadziwika anapita kwa Yesu akunjenjemera, ndipo anagwada ndi kuulula pamaso pa anthu onse chimene chinam’chititsa kuti amugwire, komanso mmene wachirira nthawi yomweyo.+