2 Mbiri 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anthuwo ananyamuka m’mawa kwambiri n’kupita kuchipululu+ cha Tekowa.+ Ali m’njira, Yehosafati anaimirira n’kunena kuti: “Tamverani inu Ayuda ndi anthu okhala mu Yerusalemu!+ Khulupirirani+ Yehova Mulungu wanu kuti mukhalitse. Khulupirirani aneneri+ ake kuti zinthu zikuyendereni bwino.” Luka 8:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Yesu atamva zimenezi, anamuyankha kuti: “Usaope, ingokhala ndi chikhulupiriro basi,+ ndipo mwana wako apulumuka.” Yohane 11:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Yesu anati: “Kodi sindinakuuze kuti ngati ukhulupirira udzaona ulemerero wa Mulungu?”+
20 Anthuwo ananyamuka m’mawa kwambiri n’kupita kuchipululu+ cha Tekowa.+ Ali m’njira, Yehosafati anaimirira n’kunena kuti: “Tamverani inu Ayuda ndi anthu okhala mu Yerusalemu!+ Khulupirirani+ Yehova Mulungu wanu kuti mukhalitse. Khulupirirani aneneri+ ake kuti zinthu zikuyendereni bwino.”
50 Yesu atamva zimenezi, anamuyankha kuti: “Usaope, ingokhala ndi chikhulupiriro basi,+ ndipo mwana wako apulumuka.”