Mateyu 19:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamenepo Petulo ananena kuti: “Taonani! Ife tasiya zinthu zonse ndi kukutsatirani, kodi tidzapeza chiyani?”+ Luka 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho ngalawazo anafika nazo kumtunda, ndipo iwo anasiya chilichonse ndi kumutsatira.+
27 Pamenepo Petulo ananena kuti: “Taonani! Ife tasiya zinthu zonse ndi kukutsatirani, kodi tidzapeza chiyani?”+