Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Nthawi yomweyo iwo anasiya maukonde awo+ n’kumutsatira.

  • Mateyu 6:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 “Chotero pitirizani kufunafuna ufumu choyamba ndi chilungamo chake,+ ndipo zina zonsezi zidzawonjezedwa kwa inu.+

  • Mateyu 19:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pamenepo Petulo ananena kuti: “Taonani! Ife tasiya zinthu zonse ndi kukutsatirani, kodi tidzapeza chiyani?”+

  • Maliko 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Nthawi yomweyo anawaitana. Iwonso anasiya bambo wawo Zebedayo m’ngalawamo limodzi ndi anthu aganyu, ndipo anam’tsatira.

  • Luka 18:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Koma Petulo ananena kuti: “Taonani! Ife tasiya zinthu zathu ndi kukutsatirani.”+

  • Afilipi 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Zoonadi, ndimaona zinthu zonse kukhala zosapindulitsa, chifukwa chakuti ndinadziwa Khristu Yesu Ambuye wanga, chimene ndi chinthu chamtengo wapatali kwambiri.+ Chifukwa cha iye, ndimaona zinthu zonse kukhala zosapindulitsa, ndipo ndimaziyesa mulu wa zinyalala,+ kuti ndikhale pa ubwenzi weniweni ndi Khristu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena