Mateyu 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musatenge thumba la chakudya cha pa ulendo, kapena malaya awiri amkati, nsapato kapena ndodo, chifukwa wantchito ayenera kulandira chakudya chake.+ Machitidwe 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno mngeloyo+ anamuuza kuti: “Konzeka ndipo uvale nsapato zako.” Iye anachita zimenezo. Kenako anamuuza kuti: “Vala malaya ako akunja+ ndipo uzinditsatira.”
10 Musatenge thumba la chakudya cha pa ulendo, kapena malaya awiri amkati, nsapato kapena ndodo, chifukwa wantchito ayenera kulandira chakudya chake.+
8 Ndiyeno mngeloyo+ anamuuza kuti: “Konzeka ndipo uvale nsapato zako.” Iye anachita zimenezo. Kenako anamuuza kuti: “Vala malaya ako akunja+ ndipo uzinditsatira.”