Esitere 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawi ina mkati mwa phwando la vinyo, mfumu inafunsa Esitere kuti: “Ukufuna kupempha chiyani?+ Chimene ukufunacho ndikupatsa. Ukufuna chiyani? Ngakhale utapempha hafu ya ufumuwu, ipatsidwa kwa iwe.” Esitere 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano mfumu inafunsanso Esitere pa tsiku lachiwiri la phwando la vinyo kuti:+ “Ukufuna kupempha chiyani+ Mfumukazi Esitere? Chimene ukufunacho ndikupatsa.+ Ukufuna chiyani? Ngakhale utapempha hafu ya ufumuwu,+ ipatsidwa kwa iwe.”
6 Pa nthawi ina mkati mwa phwando la vinyo, mfumu inafunsa Esitere kuti: “Ukufuna kupempha chiyani?+ Chimene ukufunacho ndikupatsa. Ukufuna chiyani? Ngakhale utapempha hafu ya ufumuwu, ipatsidwa kwa iwe.”
2 Tsopano mfumu inafunsanso Esitere pa tsiku lachiwiri la phwando la vinyo kuti:+ “Ukufuna kupempha chiyani+ Mfumukazi Esitere? Chimene ukufunacho ndikupatsa.+ Ukufuna chiyani? Ngakhale utapempha hafu ya ufumuwu,+ ipatsidwa kwa iwe.”