Luka 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo panali amuna pafupifupi 5,000.+ Koma Yesu anauza ophunzira ake kuti: “Auzeni akhale m’magulu, muja amakhalira akamadya chakudya. Pagulu lililonse pakhale anthu pafupifupi 50.”+
14 Pamenepo panali amuna pafupifupi 5,000.+ Koma Yesu anauza ophunzira ake kuti: “Auzeni akhale m’magulu, muja amakhalira akamadya chakudya. Pagulu lililonse pakhale anthu pafupifupi 50.”+