Maliko 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anagwira dzanja la munthu wakhunguyo, ndi kupita naye kunja kwa mudzi. Kumeneko iye analavulira+ m’maso mwake, ndi kuika manja ake pa munthuyo ndi kumufunsa kuti: “Kodi ukuona chilichonse?” Yohane 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Atanena zimenezi, analavulira malovu pansi ndi kukanda thope ndi malovuwo. Atatero anapaka thopelo m’maso mwa munthuyo.+
23 Iye anagwira dzanja la munthu wakhunguyo, ndi kupita naye kunja kwa mudzi. Kumeneko iye analavulira+ m’maso mwake, ndi kuika manja ake pa munthuyo ndi kumufunsa kuti: “Kodi ukuona chilichonse?”
6 Atanena zimenezi, analavulira malovu pansi ndi kukanda thope ndi malovuwo. Atatero anapaka thopelo m’maso mwa munthuyo.+