Mateyu 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yesu, atalowa m’nyumba mwa Petulo, anaona apongozi aakazi a Petulo+ ali gone, akudwala malungo.*+
14 Tsopano Yesu, atalowa m’nyumba mwa Petulo, anaona apongozi aakazi a Petulo+ ali gone, akudwala malungo.*+