Mateyu 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano atafika kufupi ndi khamu la anthu,+ mwamuna wina anamuyandikira, ndipo anam’gwadira ndi kunena kuti: Luka 9:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pamenepo munthu wina anafuula kuchokera m’khamulo kuti: “Mphunzitsi, ndikukupemphani kuti mukaone mwana wanga wamwamuna, chifukwa ndi mmodzi yekhayo.+
14 Tsopano atafika kufupi ndi khamu la anthu,+ mwamuna wina anamuyandikira, ndipo anam’gwadira ndi kunena kuti:
38 Pamenepo munthu wina anafuula kuchokera m’khamulo kuti: “Mphunzitsi, ndikukupemphani kuti mukaone mwana wanga wamwamuna, chifukwa ndi mmodzi yekhayo.+