Mateyu 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Ambuye, muchitire chifundo mwana wanga wamwamuna, chifukwa ndi wakhunyu ndipo akuvutika kwambiri. Amagwera pamoto kawirikawiri ndiponso amagwera m’madzi kawirikawiri.+ Maliko 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Wina m’khamulo anamuyankha kuti: “Mphunzitsi, ine ndabweretsa mwana wanga wamwamuna kwa inu chifukwa ali ndi mzimu womulepheretsa kulankhula.+ Luka 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atayandikira pachipata cha mzindawo, anakumana ndi anthu atanyamula maliro.+ Womwalirayo anali mwana wamwamuna yekhayo+ kwa mayi ake. Komanso mayi akewo anali mkazi wamasiye. Khamu lalikulu ndithu la anthu ochokera mumzindawo linali limodzi ndi mayiwo.
15 “Ambuye, muchitire chifundo mwana wanga wamwamuna, chifukwa ndi wakhunyu ndipo akuvutika kwambiri. Amagwera pamoto kawirikawiri ndiponso amagwera m’madzi kawirikawiri.+
17 Wina m’khamulo anamuyankha kuti: “Mphunzitsi, ine ndabweretsa mwana wanga wamwamuna kwa inu chifukwa ali ndi mzimu womulepheretsa kulankhula.+
12 Atayandikira pachipata cha mzindawo, anakumana ndi anthu atanyamula maliro.+ Womwalirayo anali mwana wamwamuna yekhayo+ kwa mayi ake. Komanso mayi akewo anali mkazi wamasiye. Khamu lalikulu ndithu la anthu ochokera mumzindawo linali limodzi ndi mayiwo.