Maliko 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo mzimu wonyansawo unam’tsalimitsa ndipo unafuula mokweza. Kenako unatuluka mwa munthuyo.+ Luka 9:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Koma ngakhale pamene anali kufika naye kwa iye, chiwandacho chinamugwetsa pansi ndi kum’tsalimitsa mwamphamvu. Yesu anakalipira mzimu wonyansawo ndi kuchiritsa mnyamatayo. Kenako anamupereka kwa bambo ake.+
42 Koma ngakhale pamene anali kufika naye kwa iye, chiwandacho chinamugwetsa pansi ndi kum’tsalimitsa mwamphamvu. Yesu anakalipira mzimu wonyansawo ndi kuchiritsa mnyamatayo. Kenako anamupereka kwa bambo ake.+