Mateyu 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa nthawi imeneyo, ophunzira anayandikira Yesu ndi kunena kuti: “Ndani kwenikweni amene adzakhala wamkulu kwambiri mu ufumu wakumwamba?”+ Luka 9:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Kenako iwo anayamba kukhala ndi maganizo ofuna kudziwa amene ali wamkulu koposa pakati pawo.+ Luka 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Komanso, panabuka mkangano woopsa pakati pawo za amene anali kuoneka wamkulu kwambiri.+
18 Pa nthawi imeneyo, ophunzira anayandikira Yesu ndi kunena kuti: “Ndani kwenikweni amene adzakhala wamkulu kwambiri mu ufumu wakumwamba?”+