Luka 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye atamva zimenezi, anamva chisoni kwambiri, chifukwa anali wolemera kwabasi.+