Mateyu 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mnyamata uja atamva mawu amenewa, anachoka ali wachisoni, chifukwa anali ndi katundu wambiri.+ Maliko 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma iye anakhumudwa atamva mawuwo, ndipo anachoka ali wachisoni, chifukwa anali ndi katundu wambiri.+
22 Koma iye anakhumudwa atamva mawuwo, ndipo anachoka ali wachisoni, chifukwa anali ndi katundu wambiri.+