Salimo 62:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musadalire chizolowezi chobera ena mwachinyengo,+Ndipo musakhale wachabechabe chifukwa chochita uchifwamba.+Ngati chuma chanu chachuluka, mtima wanu wonse usakhale pachumacho.+ Maliko 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma iye anakhumudwa atamva mawuwo, ndipo anachoka ali wachisoni, chifukwa anali ndi katundu wambiri.+ Luka 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye atamva zimenezi, anamva chisoni kwambiri, chifukwa anali wolemera kwabasi.+
10 Musadalire chizolowezi chobera ena mwachinyengo,+Ndipo musakhale wachabechabe chifukwa chochita uchifwamba.+Ngati chuma chanu chachuluka, mtima wanu wonse usakhale pachumacho.+
22 Koma iye anakhumudwa atamva mawuwo, ndipo anachoka ali wachisoni, chifukwa anali ndi katundu wambiri.+