Mateyu 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iwo anamuyankha kuti: “Ambuye, titseguleni maso athu.”+ Luka 18:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 “Ukufuna kuti ndikuchitire chiyani?”+ Iye anayankha kuti: “Ambuye, ndithandizeni kuti ndiyambe kuona.”+
41 “Ukufuna kuti ndikuchitire chiyani?”+ Iye anayankha kuti: “Ambuye, ndithandizeni kuti ndiyambe kuona.”+