Mateyu 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iwo anamuyankha kuti: “Ambuye, titseguleni maso athu.”+ Maliko 10:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Tsopano poyankha Yesu anamufunsa kuti: “Ukufuna kuti ndikuchitire chiyani?”+ Wakhunguyo anayankha kuti: “Rab·boʹni, ndithandizeni ndiyambe kuona.”+
51 Tsopano poyankha Yesu anamufunsa kuti: “Ukufuna kuti ndikuchitire chiyani?”+ Wakhunguyo anayankha kuti: “Rab·boʹni, ndithandizeni ndiyambe kuona.”+