Mateyu 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 n’kuwauza kuti: “Pitani m’mudzi umene mukuuonawo. Kumeneko mukapeza bulu atam’mangirira limodzi ndi mwana wake wamphongo. Mukawamasule ndi kuwabweretsa kwa ine.+ Luka 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Iye anawauza kuti: “Pitani m’mudzi umene mukuuonawo, ndipo mukalowa mmenemo mukapeza bulu wamng’ono wamphongo atamumangirira, amene munthu sanakwerepo chiyambire. Mukamumasule n’kubwera naye kuno.+
2 n’kuwauza kuti: “Pitani m’mudzi umene mukuuonawo. Kumeneko mukapeza bulu atam’mangirira limodzi ndi mwana wake wamphongo. Mukawamasule ndi kuwabweretsa kwa ine.+
30 Iye anawauza kuti: “Pitani m’mudzi umene mukuuonawo, ndipo mukalowa mmenemo mukapeza bulu wamng’ono wamphongo atamumangirira, amene munthu sanakwerepo chiyambire. Mukamumasule n’kubwera naye kuno.+