Maliko 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndi kuwauza kuti: “Pitani m’mudzi umene mukuuonawo. Mukakalowa mmenemo, mukapeza bulu wamng’ono wamphongo atam’mangirira, amene munthu sanakwerepo chiyambire. Mukam’masule ndi kubwera naye kuno.+ Luka 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Iye anawauza kuti: “Pitani m’mudzi umene mukuuonawo, ndipo mukalowa mmenemo mukapeza bulu wamng’ono wamphongo atamumangirira, amene munthu sanakwerepo chiyambire. Mukamumasule n’kubwera naye kuno.+
2 ndi kuwauza kuti: “Pitani m’mudzi umene mukuuonawo. Mukakalowa mmenemo, mukapeza bulu wamng’ono wamphongo atam’mangirira, amene munthu sanakwerepo chiyambire. Mukam’masule ndi kubwera naye kuno.+
30 Iye anawauza kuti: “Pitani m’mudzi umene mukuuonawo, ndipo mukalowa mmenemo mukapeza bulu wamng’ono wamphongo atamumangirira, amene munthu sanakwerepo chiyambire. Mukamumasule n’kubwera naye kuno.+