Mateyu 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu ambiri m’khamulo anayala malaya awo akunja+ mumsewu ndipo ena anayamba kudula nthambi za mitengo n’kuziyala mumsewu.+ Luka 19:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pamene anali kuyenda,+ anthu anali kuyala malaya awo akunja mumsewu.+
8 Anthu ambiri m’khamulo anayala malaya awo akunja+ mumsewu ndipo ena anayamba kudula nthambi za mitengo n’kuziyala mumsewu.+