Mateyu 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Yesu analowa m’kachisi ndi kuthamangitsa onse ogulitsa ndi ogula m’kachisimo, ndipo anagubuduza matebulo a osintha ndalama ndi mabenchi a ogulitsa nkhunda.+ Luka 19:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ndiyeno analowa m’kachisi n’kuyamba kuthamangitsa anthu amene anali kugulitsamo zinthu,+ Yohane 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kumeneko anapeza ogulitsa ng’ombe, nkhosa ndi nkhunda+ komanso osintha ndalama ali m’kachisi atakhala m’mipando yawo.
12 Kenako Yesu analowa m’kachisi ndi kuthamangitsa onse ogulitsa ndi ogula m’kachisimo, ndipo anagubuduza matebulo a osintha ndalama ndi mabenchi a ogulitsa nkhunda.+
14 Kumeneko anapeza ogulitsa ng’ombe, nkhosa ndi nkhunda+ komanso osintha ndalama ali m’kachisi atakhala m’mipando yawo.