Maliko 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano anafika ku Yerusalemu. Kumeneko analowa m’kachisi n’kuyamba kuthamangitsa ogula ndi ogulitsa m’kachisimo. Anagubuduza matebulo a osintha ndalama ndiponso mabenchi a ogulitsa nkhunda.+ Luka 19:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ndiyeno analowa m’kachisi n’kuyamba kuthamangitsa anthu amene anali kugulitsamo zinthu,+ Yohane 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho anapanga mkwapulo wazingwe, n’kuthamangitsa onse amene anali ndi nkhosa ndi ng’ombe ndipo anawatulutsa m’kachisimo. Anakhuthula makobidi a osintha ndalama ndi kugubuduza matebulo awo.+
15 Tsopano anafika ku Yerusalemu. Kumeneko analowa m’kachisi n’kuyamba kuthamangitsa ogula ndi ogulitsa m’kachisimo. Anagubuduza matebulo a osintha ndalama ndiponso mabenchi a ogulitsa nkhunda.+
15 Choncho anapanga mkwapulo wazingwe, n’kuthamangitsa onse amene anali ndi nkhosa ndi ng’ombe ndipo anawatulutsa m’kachisimo. Anakhuthula makobidi a osintha ndalama ndi kugubuduza matebulo awo.+