Mateyu 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno anawafunsa kuti: “Kodi nkhope iyi ndi mawu akewa n’zandani?”+ Luka 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Ndionetseni khobidi la dinari. Kodi nkhope ndi mawu ali pamenepo n’zandani?” Iwo anayankha kuti: “Ndi za Kaisara.”+
24 “Ndionetseni khobidi la dinari. Kodi nkhope ndi mawu ali pamenepo n’zandani?” Iwo anayankha kuti: “Ndi za Kaisara.”+