Luka 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma atalephera kudutsa naye chifukwa cha kuchuluka kwa anthu, anakwera padenga.* Ndipo kudzera pabowo limene anatsegula padengapo, anamutsitsa limodzi ndi kabediko n’kumufikitsa pakati pa anthu amene anali pamaso pa Yesu.+
19 Koma atalephera kudutsa naye chifukwa cha kuchuluka kwa anthu, anakwera padenga.* Ndipo kudzera pabowo limene anatsegula padengapo, anamutsitsa limodzi ndi kabediko n’kumufikitsa pakati pa anthu amene anali pamaso pa Yesu.+